Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbadwa* zako zidzakhala alendo mʼdziko la eni ndipo anthu adzazisandutsa akapolo ndi kuzizunza kwa zaka 400.+ 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wambiri.+

  • Ekisodo 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mkazi aliyense adzapemphe zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala kwa munthu wokhala naye pafupi ndi kwa mkazi amene akukhala mʼnyumba mwake. Zinthu zimenezi mudzaveke ana anu aamuna ndi ana anu aakazi, ndipo mudzatenge zinthu zambiri za Aiguputo.”+

  • Ekisodo 12:35, 36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Aisiraeli anachita zimene Mose anawauza ndipo anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide komanso zovala.+ 36 Choncho Yehova anachititsa kuti Aiguputo akomere mtima anthu ake, moti Aiguputowo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena