Ekisodo 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:35 Nsanja ya Olonda,11/1/1999, tsa. 30
35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+