Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Davide anatamanda Yehova pamaso pa mpingo wonse kuti: “Mutamandidwe inu Yehova Mulungu wa Isiraeli atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale.

  • Salimo 41:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,

      Kuyambira panopo mpaka kalekale.*+

      Ame! Ame!

  • Luka 1:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 “Atamandike Yehova* Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wakumbukira anthu ake nʼkuwabweretsera chipulumutso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena