Salimo 106:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi zambiri ankawapulumutsa,+Koma iwo ankamupandukira komanso sankamvera,+Ndipo ankawonongedwa chifukwa cha zolakwa zawo.+ Maliro 3:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Ife tachimwa komanso tapanduka+ ndipo inu simunatikhululukire.+
43 Nthawi zambiri ankawapulumutsa,+Koma iwo ankamupandukira komanso sankamvera,+Ndipo ankawonongedwa chifukwa cha zolakwa zawo.+