Salimo 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi mphamvu zanu tidzathamangitsa adani athu.+Mʼdzina lanu tidzagonjetsa anthu amene akutiukira.+