Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+ Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+
8 Ndimaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+ Chifukwa iye ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.*+