Salimo 89:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Sindidzaphwanya pangano langa+Kapena kusintha mawu otuluka pakamwa panga.+ Salimo 105:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+Lonjezo limene anapereka* ku mibadwo 1,000.+