Salimo 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo dziko lawo munalipereka kwa makolo athu.+ Munagonjetsa mitundu ya anthu nʼkuithamangitsa.+ Salimo 105:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Anatenga zinthu zimene mitundu ina ya anthu inapeza itagwira ntchito mwakhama,+
2 Munathamangitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo dziko lawo munalipereka kwa makolo athu.+ Munagonjetsa mitundu ya anthu nʼkuithamangitsa.+
44 Anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Anatenga zinthu zimene mitundu ina ya anthu inapeza itagwira ntchito mwakhama,+