Salimo 97:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 99:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi wamkulu mu Ziyoni,Ndipo iye ali pamwamba pa mitundu yonse ya anthu.+
9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+