Yesaya 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa,+Chifukwa sindingalole kuti dzina langa liipitsidwe.+ Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyense.* Yohane 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atate lemekezani dzina lanu.” Atatero mawu+ anamveka kuchokera kumwamba kuti: “Ndalilemekeza ndipo ndidzalilemekezanso.”+
11 Ndithu, ndidzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa,+Chifukwa sindingalole kuti dzina langa liipitsidwe.+ Sindipereka ulemerero wanga kwa wina aliyense.*
28 Atate lemekezani dzina lanu.” Atatero mawu+ anamveka kuchokera kumwamba kuti: “Ndalilemekeza ndipo ndidzalilemekezanso.”+