Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Komanso, Mulungu anawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi+ ndipo muziliyangʼanira.+ Muyangʼanirenso+ nsomba zamʼnyanja ndi zamoyo zouluka mumlengalenga, komanso chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.”

  • Salimo 37:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+

      Ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.+

  • Yesaya 45:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chifukwa Yehova,

      Mlengi wakumwamba,+ Mulungu woona,

      Amene anaumba dziko lapansi, amene analipanga ndi kulikhazikitsa mwamphamvu,+

      Amene sanalilenge popanda cholinga,* koma analiumba kuti anthu akhalemo,+ wanena kuti:

      “Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina.

  • Machitidwe 17:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mitundu yonse ya anthu, kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anaika nthawi yoti zinthu zina zizichitika komanso anaika malire a malo oti anthu azikhala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena