Genesis 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Komanso, Mulungu anawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi+ ndipo muziliyangʼanira.+ Muyangʼanirenso+ nsomba zamʼnyanja ndi zamoyo zouluka mumlengalenga, komanso chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.” Genesis 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake, nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke ndipo mudzaze dziko lapansi.+ Salimo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.+ Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+
28 Komanso, Mulungu anawadalitsa nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi+ ndipo muziliyangʼanira.+ Muyangʼanirenso+ nsomba zamʼnyanja ndi zamoyo zouluka mumlengalenga, komanso chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.”
9 Mulungu anadalitsa Nowa ndi ana ake, nʼkuwauza kuti: “Muberekane, muchuluke ndipo mudzaze dziko lapansi.+