Deuteronomo 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Muziyenda mʼnjira imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo, kuti zinthu zikuyendereni bwino komanso kuti mukhale ndi moyo wautali mʼdziko limene mudzalitenge kuti likhale lanu.”+ Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga, ndipo ndidzakhala Mulungu wanu, inuyo mudzakhala anthu anga.+ Muziyenda mʼnjira imene ndakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+ Yakobo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aliyense amene amamvera Chilamulo akalakwitsa mbali imodzi, ndiye kuti walakwira Chilamulo chonse.+
33 Muziyenda mʼnjira imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo, kuti zinthu zikuyendereni bwino komanso kuti mukhale ndi moyo wautali mʼdziko limene mudzalitenge kuti likhale lanu.”+
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga, ndipo ndidzakhala Mulungu wanu, inuyo mudzakhala anthu anga.+ Muziyenda mʼnjira imene ndakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
10 Aliyense amene amamvera Chilamulo akalakwitsa mbali imodzi, ndiye kuti walakwira Chilamulo chonse.+