Yesaya 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, ndipulumutseni,Ndipo ine ndi anthu ena tidzaimba nyimbo zanga ndi zoimbira za zingwe+Kunyumba ya Yehova masiku onse a moyo wathu.’”+
20 Inu Yehova, ndipulumutseni,Ndipo ine ndi anthu ena tidzaimba nyimbo zanga ndi zoimbira za zingwe+Kunyumba ya Yehova masiku onse a moyo wathu.’”+