Salimo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tetezani moyo wanga ndipo mundipulumutse.+ Musalole kuti ndichite manyazi, chifukwa ndathawira kwa inu. Salimo 119:80 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Mtima wanga uzitsatira malangizo anu mosalakwitsa kanthu,+Kuti ndisachite manyazi.+
20 Tetezani moyo wanga ndipo mundipulumutse.+ Musalole kuti ndichite manyazi, chifukwa ndathawira kwa inu.