Salimo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya. Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+ Salimo 119:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Inu Yehova, ndikudziwa kuti zigamulo zanu ndi zolungama+Komanso kuti mwandilanga chifukwa chakuti ndinu wokhulupirika.+
9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya. Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+
75 Inu Yehova, ndikudziwa kuti zigamulo zanu ndi zolungama+Komanso kuti mwandilanga chifukwa chakuti ndinu wokhulupirika.+