Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndimakukumbukirani ndili pabedi langa,Ndimaganizira mozama za inu usiku wonse.*+ Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+
9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+