Salimo 119:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Usiku ndimakumbukira dzina lanu, inu Yehova,+Kuti ndisunge chilamulo chanu. Salimo 119:148 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 148 Ndimadzuka pakati pa usiku,*Kuti ndiganizire mozama* mawu anu.+