Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndimakukumbukirani ndili pabedi langa,Ndimaganizira mozama za inu usiku wonse.*+ Luka 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mʼmasiku amenewo, Yesu anapita kuphiri kukapemphera+ ndipo anachezera usiku wonse kupemphera kwa Mulungu.+
12 Mʼmasiku amenewo, Yesu anapita kuphiri kukapemphera+ ndipo anachezera usiku wonse kupemphera kwa Mulungu.+