Salimo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye amakonda chilungamo ndipo amaweruza mosakondera.+ Dziko lapansi ladzaza ndi chikondi chokhulupirika cha Yehova.+ Salimo 104:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu amathirira mapiri kuchokera mʼzipinda zake zamʼmwamba.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zipatso za ntchito zanu.+
5 Iye amakonda chilungamo ndipo amaweruza mosakondera.+ Dziko lapansi ladzaza ndi chikondi chokhulupirika cha Yehova.+
13 Mulungu amathirira mapiri kuchokera mʼzipinda zake zamʼmwamba.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zipatso za ntchito zanu.+