Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 51:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+

      Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+

  • Salimo 103:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mofanana ndi bambo amene amasonyeza chifundo kwa ana ake,

      Yehova wasonyezanso chifundo kwa anthu amene amamuopa.+

  • Salimo 119:116
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 116 Inu Mulungu, ndithandizeni mogwirizana ndi zimene munalonjeza,*+

      Kuti ndikhalebe ndi moyo.

      Musalole kuti ndichite manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.*+

  • Danieli 9:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Inu Mulungu wanga, tcherani khutu lanu kuti mumve. Tsegulani maso anu kuti muone zimene zatichitikira komanso mmene mzinda wodziwika ndi dzina lanu wawonongekera. Ifeyo sitikukuchondererani chifukwa choti tachita zinthu zolungama ayi, koma chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+

  • Luka 1:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Kumibadwomibadwo iye amachitira chifundo anthu amene amamuopa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena