Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Muzisunga malamulo anga ndi zigamulo zanga. Aliyense amene akuchita zimenezi adzakhala ndi moyo chifukwa cha malamulo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.

  • Deuteronomo 30:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mukadzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani lero, pokonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda mʼnjira zake ndi kusunga malamulo ake, malangizo ake ndi zigamulo zake, mudzakhala ndi moyo,+ mudzachulukana ndipo Yehova Mulungu wanu adzakudalitsani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.+

  • Yohane 6:63
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo+ koma mnofu ulibe ntchito iliyonse. Mawu amene ndakuuzaniwa ndi mzimu ndiponso ndi moyo.+

  • Aroma 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pajatu Mose analemba zokhudza mmene munthu angachitire chilungamo mogwirizana ndi Chilamulo, anati: “Aliyense amene akuchita zimenezi adzakhala ndi moyo chifukwa cha malamulo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena