1 Mafumu 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Eliya anayandikira anthu onsewo nʼkunena kuti: “Kodi mukayikakayika mpaka liti?+ Ngati Yehova ali Mulungu woona mʼtsatireni,+ koma ngati Mulungu woona ndi Baala tsatirani ameneyo.” Koma anthuwo sanamuyankhe chilichonse. Chivumbulutso 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma chifukwa choti ndiwe wofunda, osati wotentha+ kapena wozizira,+ ndikulavula mʼkamwa mwanga.
21 Kenako Eliya anayandikira anthu onsewo nʼkunena kuti: “Kodi mukayikakayika mpaka liti?+ Ngati Yehova ali Mulungu woona mʼtsatireni,+ koma ngati Mulungu woona ndi Baala tsatirani ameneyo.” Koma anthuwo sanamuyankhe chilichonse.