-
Salimo 119:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Ndithandizeni kuti ndikhale wozindikira
Kuti nditsatire chilamulo chanu,
Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wanga wonse.
-
-
2 Timoteyo 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Nthawi zonse uziganizira zimene ndikukuuzazi ndipo Ambuye adzakuthandiza kumvetsa zinthu zonse.
-