Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo mundiletse kuchita zinthu modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+ Mukatero ndidzakhala wopanda chifukwa,+Komanso ndidzakhala wopanda mlandu wa machimo akuluakulu.* Aroma 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe ngati mfumu mʼmatupi anu oti akhoza kufawo+ kuti muzitsatira zilakolako zawo.
13 Ndipo mundiletse kuchita zinthu modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+ Mukatero ndidzakhala wopanda chifukwa,+Komanso ndidzakhala wopanda mlandu wa machimo akuluakulu.*
12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe ngati mfumu mʼmatupi anu oti akhoza kufawo+ kuti muzitsatira zilakolako zawo.