Aroma 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2016, tsa. 10
12 Choncho musalole kuti uchimo uzilamulirabe monga mfumu+ m’matupi anu okhoza kufawo kuti muzitsatira zilakolako zawo.+