Numeri 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova asonyeze kuti akusangalala nanu+ ndipo akukomereni mtima. Salimo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndi ndani amene adzationetse chinthu chabwino chilichonse?” Inu Yehova, kuwala kwa nkhope yanu kutiunikire.+
6 Pali ambiri amene akunena kuti: “Ndi ndani amene adzationetse chinthu chabwino chilichonse?” Inu Yehova, kuwala kwa nkhope yanu kutiunikire.+