Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 6:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Yehova akuyangʼaneni mokondwera ndipo akupatseni mtendere.”’+

  • Salimo 80:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba, tibwezeretseni mwakale.

      Walitsani nkhope yanu pa ife kuti tipulumutsidwe.+

  • Miyambo 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.

      Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+

  • 1 Petulo 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Maso a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva mapemphero awo opembedzera,+ koma Yehova* amakwiyira anthu amene amachita zoipa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena