Salimo 119:144 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 144 Zikumbutso zanu zidzakhalabe zolungama mpaka kalekale. Ndithandizeni kukhala wozindikira+ kuti ndikhalebe ndi moyo. Mlaliki 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndazindikira kuti zonse zimene Mulungu woona amapanga zidzakhalapo mpaka kalekale. Palibe choti nʼkuwonjezerapo kapena kuchotsapo. Mulungu woona anazipanga mwanjira imeneyi kuti anthu azimuopa.+
144 Zikumbutso zanu zidzakhalabe zolungama mpaka kalekale. Ndithandizeni kukhala wozindikira+ kuti ndikhalebe ndi moyo.
14 Ndazindikira kuti zonse zimene Mulungu woona amapanga zidzakhalapo mpaka kalekale. Palibe choti nʼkuwonjezerapo kapena kuchotsapo. Mulungu woona anazipanga mwanjira imeneyi kuti anthu azimuopa.+