Salimo 119:144 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 144 Zikumbutso zanu zidzakhalabe zolungama mpaka kalekale.+Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti ndikhalebe ndi moyo.+
144 Zikumbutso zanu zidzakhalabe zolungama mpaka kalekale.+Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti ndikhalebe ndi moyo.+