Salimo 119:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti nditsatire chilamulo chanu,+Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wonse.+ Salimo 119:116 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 116 Inu Mulungu, ndithandizeni monga mwa mawu anu kuti ndikhalebe ndi moyo,+Ndipo musandichititse manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.+ Miyambo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Milomo ya wolungama imaweta anthu ambiri,+ koma zitsiru zimafa chifukwa chopanda nzeru mumtima.+ Danieli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+
34 Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti nditsatire chilamulo chanu,+Ndiponso kuti ndichisunge ndi mtima wonse.+
116 Inu Mulungu, ndithandizeni monga mwa mawu anu kuti ndikhalebe ndi moyo,+Ndipo musandichititse manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.+
10 Anthu ambiri adzadzitsuka,+ adzadziyeretsa+ ndipo adzayengedwa.+ Anthu oipa adzachita zinthu zoipa+ ndipo palibe munthu woipa aliyense amene adzamvetsetse mawu amenewa,+ koma anthu ozindikira adzawamvetsetsa.+