Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+

      Musalole kuti ndichite manyazi.

      Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+

  • Yesaya 45:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma Isiraeli adzapulumutsidwa chifukwa chokhala pa mgwirizano ndi Yehova+ ndipo adzakhala wopulumutsidwa mpaka kalekale.+ Anthu inu simudzachita manyazi+ ndipo simudzanyozeka+ mpaka kalekale, ngakhale kwamuyaya.

  • Aroma 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 ndipo chiyembekezocho sichitikhumudwitsa+ chifukwa Mulungu wadzaza chikondi chake+ m’mitima yathu+ kudzera mwa mzimu woyera+ umene tinapatsidwa.

  • Aroma 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Paja Lemba limati: “Palibe wokhulupirira iye,+ amene adzakhumudwe.”+

  • 1 Petulo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Lemba limati: “Inetu ndikuika mwala m’Ziyoni, mwala wochita kusankhidwa mwapadera, wapakona pa maziko, wamtengo wapatali, ndipo aliyense woukhulupirira sadzakhumudwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena