1 Mbiri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso mphamvu zotsogolera Aisiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+ Miyambo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso ukapempha kuti ukhale womvetsa zinthu+Ndi kuchonderera kuti ukhale wozindikira,+ Miyambo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Udzamvetsa tanthauzo la kuopa Yehova+Ndipo udzamudziwadi Mulungu.+
12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso mphamvu zotsogolera Aisiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+
3 Komanso ukapempha kuti ukhale womvetsa zinthu+Ndi kuchonderera kuti ukhale wozindikira,+ Miyambo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Udzamvetsa tanthauzo la kuopa Yehova+Ndipo udzamudziwadi Mulungu.+