Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa kuzungulira anthu onse amene amaopa Mulungu,+

      Ndipo amawapulumutsa.+

  • Yesaya 31:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mofanana ndi mbalame imene imauluka kuti iteteze ana ake, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzateteza mzinda wa Yerusalemu.+

      Iye adzauteteza nʼkuupulumutsa.

      Adzaonetsetsa kuti usawonongedwe ndipo adzaulanditsa.”

  • Zekariya 2:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mngeloyo anauza mnzakeyo kuti: “Thamanga ukauze mnyamata uyo kuti, ‘“Mu Yerusalemu anthu azidzakhalamo+ ngati mzinda wopanda mpanda chifukwa cha anthu onse ndiponso ziweto zimene zili mmenemo.+ 5 Ine ndidzakhala ngati mpanda wake wamoto+ ndipo ulemerero wanga udzadzaza mumzindawu,”’+ watero Yehova.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena