Numeri 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nthawi zonse Likasa likamanyamuka, Mose ankanena kuti: “Nyamukani, inu Yehova,+ adani anu abalalike. Ndipo amene amadana nanu athawe pamaso panu.” 2 Samueli 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anaika Likasa la Yehova pamalo ake mutenti imene Davide anamanga.+ Ndiyeno Davide anapereka kwa Yehova+ nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+
35 Nthawi zonse Likasa likamanyamuka, Mose ankanena kuti: “Nyamukani, inu Yehova,+ adani anu abalalike. Ndipo amene amadana nanu athawe pamaso panu.”
17 Kenako anaika Likasa la Yehova pamalo ake mutenti imene Davide anamanga.+ Ndiyeno Davide anapereka kwa Yehova+ nsembe zopsereza+ ndi nsembe zamgwirizano.+