Numeri 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nthawi zonse likasa likamanyamuka, Mose anali kunena kuti: “Nyamukani, inu Yehova, adani anu abalalike.+ Ndipo amene ali nanu chidani chachikulu athawe patsogolo panu.”+
35 Nthawi zonse likasa likamanyamuka, Mose anali kunena kuti: “Nyamukani, inu Yehova, adani anu abalalike.+ Ndipo amene ali nanu chidani chachikulu athawe patsogolo panu.”+