Salimo 68:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Mulungu anyamuke,+ adani ake amwazike,+Ndipo amene amadana naye kwambiri athawe pamaso pake.+