-
Salimo 59:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Musawaphe, kuti anthu a mtundu wanga angaiwale.+
Ndi mphamvu zanu zochuluka achititseni kuyendayenda,+
Ndipo agwetseni, inu Yehova, chishango chathu,+
-