Genesis 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uziti ukalima, nthaka sizikubalira mokwanira.+ Udzakhala moyo woyendayenda ndi wothawathawa padziko lapansi.”+ Ezekieli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
12 Uziti ukalima, nthaka sizikubalira mokwanira.+ Udzakhala moyo woyendayenda ndi wothawathawa padziko lapansi.”+
15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+