Salimo 59:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musawaphe, kuti anthu a mtundu wanga asaiwale. Ndi mphamvu zanu achititseni kuti aziyendayenda,Achititseni kuti agwe, inu Yehova, chishango chathu.+
11 Musawaphe, kuti anthu a mtundu wanga asaiwale. Ndi mphamvu zanu achititseni kuti aziyendayenda,Achititseni kuti agwe, inu Yehova, chishango chathu.+