Genesis 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+ Deuteronomo 33:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”* Salimo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma inu Yehova, mumanditeteza mbali zonse+ ngati chishango,Ndinu ulemerero wanga+ komanso ndinu amene mumatukula mutu wanga.+
15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+
29 Ndiwe wosangalala iwe Isiraeli!+ Ndani angafanane ndi iwe,+Anthu amene akupulumutsidwa ndi Yehova,+Chishango chako chokuteteza,+Komanso lupanga lako lamphamvu? Adani ako adzakhala mwamantha chifukwa cha iwe,+Ndipo iwe udzaponda pamisana yawo.”*
3 Koma inu Yehova, mumanditeteza mbali zonse+ ngati chishango,Ndinu ulemerero wanga+ komanso ndinu amene mumatukula mutu wanga.+