Salimo 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+ Salimo 68:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Mulungu anyamuke,+ adani ake amwazike,+Ndipo amene amadana naye kwambiri athawe pamaso pake.+ Yesaya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mitundu ya anthu+ idzasokosera ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula,+ ndipo iwo adzathawira kutali. Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo m’mapiri ndiponso adzauluzika ngati tizitsotso touluzika ndi mphepo yamkuntho.+
6 Mitundu ya anthu inachita phokoso,+ maufumu anagwedezeka.Iye anatulutsa mawu ndipo dziko lapansi linasungunuka.+
13 Mitundu ya anthu+ idzasokosera ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula,+ ndipo iwo adzathawira kutali. Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo m’mapiri ndiponso adzauluzika ngati tizitsotso touluzika ndi mphepo yamkuntho.+