Deuteronomo 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 koma wobwezera munthu wodana ndi Mulunguyo mwa kumuwononga+ pamasom’pamaso. Sadzazengereza kuwononga munthu amene amadana ndi Mulungu. Adzam’bwezera pamasom’pamaso. Salimo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dzanja lanu lidzapeza adani anu onse.+Dzanja lanu lamanja lidzapeza odana nanu.
10 koma wobwezera munthu wodana ndi Mulunguyo mwa kumuwononga+ pamasom’pamaso. Sadzazengereza kuwononga munthu amene amadana ndi Mulungu. Adzam’bwezera pamasom’pamaso.