Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+ Yesaya 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu ya anthu yathawa itamva mkokomo wa mawu anu.+ Mitundu yamwazikana chifukwa chakuti inu mwanyamuka.+
5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+
3 Mitundu ya anthu yathawa itamva mkokomo wa mawu anu.+ Mitundu yamwazikana chifukwa chakuti inu mwanyamuka.+