Numeri 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Nthawi zonse likasa likamanyamuka, Mose anali kunena kuti: “Nyamukani, inu Yehova, adani anu abalalike.+ Ndipo amene ali nanu chidani chachikulu athawe patsogolo panu.”+ Salimo 44:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nyamukani kuti mutithandize+Tiwomboleni chifukwa cha kukoma mtima kwanu kosatha.+
35 Nthawi zonse likasa likamanyamuka, Mose anali kunena kuti: “Nyamukani, inu Yehova, adani anu abalalike.+ Ndipo amene ali nanu chidani chachikulu athawe patsogolo panu.”+