Salimo 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ine ndidzayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+Ndiwomboleni+ ndi kundikomera mtima.+ Salimo 130:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+
11 Koma ine ndidzayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+Ndiwomboleni+ ndi kundikomera mtima.+
7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+