Salimo 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikayangʼana kumwamba, ntchito ya zala zanu,Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+