1 Mafumu 8:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ansembe atatuluka mʼmalo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.+ 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo analephera kutumikira popeza ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
10 Ansembe atatuluka mʼmalo oyera, mtambo+ unadzaza nyumba ya Yehova.+ 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo analephera kutumikira popeza ulemerero wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+