Salimo 52:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Nʼchifukwa chiyani ukudzitukumula chifukwa cha zinthu zoipa zimene ukuchita, wamphamvu iwe?+ Chikondi chokhulupirika cha Mulungu nʼchokhalitsa.+ 2 Lilime lako limene ndi lakuthwa ngati lezala,+Limakonza chiwembu komanso kuchita zachinyengo.+ Salimo 58:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Oipa amasochera* akangobadwa.*Iwo amakhala osamvera komanso abodza kuchokera nthawi imene anabadwa. 4 Iwo ali ndi poizoni ngati wa njoka.+Ndipo ndi ogontha ngati njoka ya mamba imene yatseka makutu ake.
52 Nʼchifukwa chiyani ukudzitukumula chifukwa cha zinthu zoipa zimene ukuchita, wamphamvu iwe?+ Chikondi chokhulupirika cha Mulungu nʼchokhalitsa.+ 2 Lilime lako limene ndi lakuthwa ngati lezala,+Limakonza chiwembu komanso kuchita zachinyengo.+
3 Oipa amasochera* akangobadwa.*Iwo amakhala osamvera komanso abodza kuchokera nthawi imene anabadwa. 4 Iwo ali ndi poizoni ngati wa njoka.+Ndipo ndi ogontha ngati njoka ya mamba imene yatseka makutu ake.