Salimo 140:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anola lilime lawo ndipo lakhala ngati la njoka.+Mʼmilomo yawo muli poizoni wa mphiri.+ (Selah) Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma palibe munthu amene angathe kuweta lilime. Lilime ndi losalamulirika ndipo limavulaza komanso ndi lodzaza ndi poizoni wakupha.+
8 Koma palibe munthu amene angathe kuweta lilime. Lilime ndi losalamulirika ndipo limavulaza komanso ndi lodzaza ndi poizoni wakupha.+